-
2 Mafumu 7:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Choncho akhatewo anapita nʼkukafuulira alonda apageti la mzinda kuti: “Tinapita kumsasa wa Asiriya koma tapeza kuti kulibe anthu ndipo sikukumveka mawu a munthu aliyense! Kuli mahatchi ndi abulu omangidwa, komanso matenti angowasiya mmene analili!”
-