-
2 Mafumu 7:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Mfumuyo itangomva inadzuka usikuwo ndipo inauza atumiki ake kuti: “Tadikirani ndikuuzeni zimene Asiriyawa achita. Akudziwa kuti ife tili ndi njala,+ choncho achoka mumsasamo nʼkukabisala kutchire. Maganizo awo ndi akuti, ‘Atuluka mumzindamo ndipo tiwagwira amoyo. Kenako ifeyo tikalowa mumzindamo.’”+
-