-
2 Mafumu 7:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Ndiyeno mtumiki wina wa mfumu anati: “Uzani anthu atenge mahatchi 5 pa mahatchi amene atsala mumzindawu ndipo muwatume akaone. Zimene zingakawachitikire anthuwo sizingasiyane ndi zimene zichitikire gulu la Aisiraeli amene atsala mumzindamu. Komanso sizingasiyane ndi zimene zachitikira gulu la Aisiraeli amene afa.”
-