-
2 Mafumu 7:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Koma msilikali wothandiza mfumu uja anayankha munthu wa Mulungu woonayo kuti: “Ngakhale Yehova atatsegula zotsekera madzi akumwamba, kodi zimenezi zingachitike?” Ndiyeno Elisa anati: “Uona zimenezi ndi maso ako, koma sudya nawo.”
-