2 Mafumu 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Choncho mayiyo ndi banja lake ananyamuka nʼkupita kukakhala mʼdziko la Afilisiti+ kwa zaka 7, mogwirizana ndi zimene munthu wa Mulungu woonayo ananena.
2 Choncho mayiyo ndi banja lake ananyamuka nʼkupita kukakhala mʼdziko la Afilisiti+ kwa zaka 7, mogwirizana ndi zimene munthu wa Mulungu woonayo ananena.