-
2 Mafumu 8:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Zaka 7 zitatha, mayiyo anabwerera kuchokera kudziko la Afilisiti nʼkupita kukapempha mfumu kuti imubwezere nyumba yake ndi munda wake.
-