-
2 Mafumu 8:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Elisa anayangʼanitsitsa Hazaeli mpaka Hazaeliyo anachita manyazi. Kenako munthu wa Mulungu woonayo anayamba kulira.
-