2 Mafumu 8:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako Hazaeli anachoka kwa Elisa nʼkubwerera kwa mbuye wake ndipo iye anamufunsa kuti: “Kodi Elisa wakuuza kuti chiyani?” Hazaeli anayankha kuti: “Wandiuza kuti, ‘Muchira ndithu.’”+
14 Kenako Hazaeli anachoka kwa Elisa nʼkubwerera kwa mbuye wake ndipo iye anamufunsa kuti: “Kodi Elisa wakuuza kuti chiyani?” Hazaeli anayankha kuti: “Wandiuza kuti, ‘Muchira ndithu.’”+