2 Mafumu 8:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mʼmasiku a Yehoramu, Aedomu anagalukira Yuda+ ndipo kenako anasankha mfumu yoti iziwalamulira.+