-
2 Mafumu 9:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Atafika mumzindawo, anapeza akuluakulu a asilikali atakhalakhala. Kenako iye anati: “Ndabwera ndi uthenga wanu inu mkulu wa asilikali.” Ndiyeno Yehu anati: “Ndani kwenikweni pakati pathupa?” Iye anayankha kuti: “Inuyo mkulu wa asilikali.”
-