2 Mafumu 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho Yehu ananyamuka nʼkulowa mʼnyumba. Ndiyeno mtumiki wa mneneri uja anatenga mafuta aja nʼkumuthira pamutu. Kenako anamuuza kuti: “Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Ndikukudzoza kuti ukhale mfumu ya anthu a Yehova, Aisiraeli.+
6 Choncho Yehu ananyamuka nʼkulowa mʼnyumba. Ndiyeno mtumiki wa mneneri uja anatenga mafuta aja nʼkumuthira pamutu. Kenako anamuuza kuti: “Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Ndikukudzoza kuti ukhale mfumu ya anthu a Yehova, Aisiraeli.+