2 Mafumu 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Yezebeli adzadyedwa ndi agalu mʼmunda wa ku Yezereeli+ ndipo palibe amene adzamuike mʼmanda.’” Mtumikiyo atamaliza kunena zimenezi, anatsegula chitseko nʼkuthawa.+
10 Yezebeli adzadyedwa ndi agalu mʼmunda wa ku Yezereeli+ ndipo palibe amene adzamuike mʼmanda.’” Mtumikiyo atamaliza kunena zimenezi, anatsegula chitseko nʼkuthawa.+