2 Mafumu 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma iwo anati: “Ayi ukunama! Tiuze zoona.” Ndiyeno Yehu anati: “Wandiuza zakutizakuti kenako ananena kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Ndikukudzoza kuti ukhale mfumu ya Isiraeli.”’”+
12 Koma iwo anati: “Ayi ukunama! Tiuze zoona.” Ndiyeno Yehu anati: “Wandiuza zakutizakuti kenako ananena kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Ndikukudzoza kuti ukhale mfumu ya Isiraeli.”’”+