2 Mafumu 9:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Anthuwo atamva zimenezi, nthawi yomweyo aliyense anavula malaya ake nʼkumuyalira pamasitepe popanda kanthu.+ Kenako analiza malipenga nʼkunena kuti: “Tsopano Yehu ndi mfumu!”+
13 Anthuwo atamva zimenezi, nthawi yomweyo aliyense anavula malaya ake nʼkumuyalira pamasitepe popanda kanthu.+ Kenako analiza malipenga nʼkunena kuti: “Tsopano Yehu ndi mfumu!”+