-
2 Mafumu 9:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Choncho anatumizanso munthu wina wokwera pahatchi. Nayenso atafika anati: “Mfumu yanena kuti, ‘Kodi mukubwerera zamtendere?’” Koma Yehu anati: “Ukudziwa chiyani zokhudza ‘mtendereʼ iweyo? Tiye zinditsatira!”
-