-
2 Mafumu 9:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Ndiyeno Yehoramu anatembenuza galeta lake kuti azithawa ndipo anauza Ahaziya kuti: “Ahaziya, anthuwa atikonzera chiwembu!”
-