2 Mafumu 9:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndiyeno Yehu atalowa pageti, Yezebeli anati: “Kodi Zimiri amene anapha mbuye wake, zinthu zinamuyendera bwino?”+
31 Ndiyeno Yehu atalowa pageti, Yezebeli anati: “Kodi Zimiri amene anapha mbuye wake, zinthu zinamuyendera bwino?”+