-
2 Mafumu 10:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 musankhe mwana mmodzi woyenera ndiponso wabwino pakati pa ana aamuna a mbuye wanu, nʼkumuika pampando wachifumu wa bambo ake. Kenako mumenyere nkhondo nyumba ya mbuye wanu.”
-