2 Mafumu 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma iwo atamva zimenezi anachita mantha kwambiri ndipo anati: “Mafumu awiri sanathe kulimbana naye,+ ndiye ife tingalimbane naye?”
4 Koma iwo atamva zimenezi anachita mantha kwambiri ndipo anati: “Mafumu awiri sanathe kulimbana naye,+ ndiye ife tingalimbane naye?”