-
2 Mafumu 10:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Munthu wina anapita kwa Yehu kukamuuza kuti: “Mitu ya ana a mfumu ija abwera nayo.” Yehu anati: “Kaiunjikeni milu iwiri pageti la mzinda ndipo ikhale pompo mpaka mʼmawa.”
-