2 Mafumu 10:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Komanso Yehu anasonkhanitsa anthu onse nʼkuwauza kuti: “Ahabu ankalambira Baala pangʼono+ koma Yehu alambira Baala kwambiri.
18 Komanso Yehu anasonkhanitsa anthu onse nʼkuwauza kuti: “Ahabu ankalambira Baala pangʼono+ koma Yehu alambira Baala kwambiri.