2 Mafumu 10:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kenako Yehu ndi Yehonadabu+ mwana wa Rekabu analowa mʼkachisimo. Ndiyeno Yehu anauza anthu olambira Baala kuti: “Fufuzani mosamala ndipo muonetsetse kuti muno mulibe aliyense wolambira Yehova, koma olambira Baala okhaokha.”
23 Kenako Yehu ndi Yehonadabu+ mwana wa Rekabu analowa mʼkachisimo. Ndiyeno Yehu anauza anthu olambira Baala kuti: “Fufuzani mosamala ndipo muonetsetse kuti muno mulibe aliyense wolambira Yehova, koma olambira Baala okhaokha.”