-
2 Mafumu 10:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Zitatero, iwo anabwera kudzapereka nsembe zopsereza ndi nsembe zina. Yehu anali ataika amuna 80 panja nʼkuwauza kuti: “Aliyense amene athawitse munthu, pa anthu amene ndikuwapereka mʼmanja mwanu, moyo wake ulowa mʼmalo mwa munthuyo.”
-