-
2 Mafumu 11:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Mudzazungulire mfumuyo kumbali zonse mutatenga zida ndipo aliyense wofuna kudutsa pakati panu, adzaphedwe. Muzidzateteza mfumuyo kulikonse kumene ingapite.”
-