2 Mafumu 11:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Atsogoleri a magulu a asilikali 100+ anachitadi zimene wansembe Yehoyada analamula. Choncho, aliyense anatenga asilikali ake amene ankagwira ntchito pa Sabata ndi amene ankafunika kupuma pa Sabata, nʼkupita kwa wansembe Yehoyada.+
9 Atsogoleri a magulu a asilikali 100+ anachitadi zimene wansembe Yehoyada analamula. Choncho, aliyense anatenga asilikali ake amene ankagwira ntchito pa Sabata ndi amene ankafunika kupuma pa Sabata, nʼkupita kwa wansembe Yehoyada.+