2 Mafumu 11:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Asilikali olondera nyumba yachifumu+ anaima pamalo awo, aliyense atanyamula zida zake, kuyambira kumanja kwa nyumbayo mpaka kumanzere kwa nyumbayo, pafupi ndi guwa lansembe+ ndiponso pafupi ndi nyumbayo. Anazungulira mfumuyo kumbali zonse.
11 Asilikali olondera nyumba yachifumu+ anaima pamalo awo, aliyense atanyamula zida zake, kuyambira kumanja kwa nyumbayo mpaka kumanzere kwa nyumbayo, pafupi ndi guwa lansembe+ ndiponso pafupi ndi nyumbayo. Anazungulira mfumuyo kumbali zonse.