2 Mafumu 11:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiyeno Yehoyada anachita pangano pakati pa Yehova, mfumu ndi anthu,+ kuti iwo apitiriza kukhala anthu a Yehova. Anachitanso pangano pakati pa mfumu ndi anthuwo.+
17 Ndiyeno Yehoyada anachita pangano pakati pa Yehova, mfumu ndi anthu,+ kuti iwo apitiriza kukhala anthu a Yehova. Anachitanso pangano pakati pa mfumu ndi anthuwo.+