2 Mafumu 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho Mfumu Yehoasi anaitana wansembe Yehoyada+ ndi ansembe ena nʼkuwafunsa kuti: “Nʼchifukwa chiyani simukukonza nyumbayi? Ndiye musatengenso ndalama zina kwa anthu omwe apereka, pokhapokha ngati mungazigwiritse ntchito pokonza nyumbayi.”+
7 Choncho Mfumu Yehoasi anaitana wansembe Yehoyada+ ndi ansembe ena nʼkuwafunsa kuti: “Nʼchifukwa chiyani simukukonza nyumbayi? Ndiye musatengenso ndalama zina kwa anthu omwe apereka, pokhapokha ngati mungazigwiritse ntchito pokonza nyumbayi.”+