2 Mafumu 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma ndalama zimene anthu ankabweretsa kunyumba ya Yehova sanazigwiritse ntchito popanga mabeseni asiliva, zozimitsira nyale, mbale zolowa, malipenga+ ndiponso ziwiya zilizonse zagolide kapena zasiliva za mʼnyumba ya Yehova.+
13 Koma ndalama zimene anthu ankabweretsa kunyumba ya Yehova sanazigwiritse ntchito popanga mabeseni asiliva, zozimitsira nyale, mbale zolowa, malipenga+ ndiponso ziwiya zilizonse zagolide kapena zasiliva za mʼnyumba ya Yehova.+