2 Mafumu 12:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma ndalama za nsembe zakupalamula+ ndi za nsembe zamachimo sankazipereka kuti zigwire ntchito yokonzetsera nyumba ya Yehova chifukwa zinali za ansembe.+
16 Koma ndalama za nsembe zakupalamula+ ndi za nsembe zamachimo sankazipereka kuti zigwire ntchito yokonzetsera nyumba ya Yehova chifukwa zinali za ansembe.+