2 Mafumu 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mʼchaka cha 23 cha Yehoasi+ mwana wa Ahaziya+ mfumu ya Yuda, Yehoahazi mwana wa Yehu+ anakhala mfumu ya Isiraeli ku Samariya ndipo analamulira kwa zaka 17.
13 Mʼchaka cha 23 cha Yehoasi+ mwana wa Ahaziya+ mfumu ya Yuda, Yehoahazi mwana wa Yehu+ anakhala mfumu ya Isiraeli ku Samariya ndipo analamulira kwa zaka 17.