2 Mafumu 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Patapita nthawi Yehoahazi anachonderera Yehova kuti awachitire chifundo ndipo Yehova anamumvera, chifukwa anaona kuti mfumu ya Siriya inkapondereza Aisiraeli.+
4 Patapita nthawi Yehoahazi anachonderera Yehova kuti awachitire chifundo ndipo Yehova anamumvera, chifukwa anaona kuti mfumu ya Siriya inkapondereza Aisiraeli.+