2 Mafumu 13:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iye anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova. Sanasiye kuchita machimo onse amene Aisiraeli ankachita chifukwa cha Yerobowamu mwana wa Nebati.+ Iye anapitiriza kuchita machimowo.
11 Iye anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova. Sanasiye kuchita machimo onse amene Aisiraeli ankachita chifukwa cha Yerobowamu mwana wa Nebati.+ Iye anapitiriza kuchita machimowo.