-
2 Mafumu 13:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Kenako iye anauza mfumu ya Isiraeliyo kuti: “Gwirani utawo.” Mfumuyo inaugwiradi ndipo Elisa anaika manja ake pamanja a mfumuyo.
-