-
2 Mafumu 13:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Ananenanso kuti: “Tengani miviyo,” ndipo iye anaitengadi. Ndiyeno Elisa anauza mfumu ya Isiraeli kuti: “Menyani pansi ndi miviyo.” Mfumuyo inamenya katatu nʼkusiya.
-