2 Mafumu 13:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Munthu wa Mulungu woonayo anakwiyira mfumuyo kwambiri, ndipo anati: “Munayenera kumenya maulendo 5 kapena 6! Mukanatero mukanaphadi Asiriya mpaka kuwamaliza, koma apa mudzawagonjetsa katatu kokha.”+
19 Munthu wa Mulungu woonayo anakwiyira mfumuyo kwambiri, ndipo anati: “Munayenera kumenya maulendo 5 kapena 6! Mukanatero mukanaphadi Asiriya mpaka kuwamaliza, koma apa mudzawagonjetsa katatu kokha.”+