2 Mafumu 14:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Amaziya anapha Aedomu+ okwana 10,000 mʼchigwa cha Mchere+ nʼkulanda mzinda wa Sela pa nkhondo.+ Mzindawo anaupatsa dzina lakuti Yokiteeli ndipo dzina lake ndi lomweli mpaka lero.
7 Amaziya anapha Aedomu+ okwana 10,000 mʼchigwa cha Mchere+ nʼkulanda mzinda wa Sela pa nkhondo.+ Mzindawo anaupatsa dzina lakuti Yokiteeli ndipo dzina lake ndi lomweli mpaka lero.