2 Mafumu 14:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chifukwa chakuti wagonjetsa Edomu,+ wayamba kukula mtima. Sangalala ndi ulemerero umene wapeza ndipo khala mʼnyumba* mwako momwemo. Nʼchifukwa chiyani ukuputa tsoka chonsecho iwe ndi Ayudawo mugonja?”
10 Chifukwa chakuti wagonjetsa Edomu,+ wayamba kukula mtima. Sangalala ndi ulemerero umene wapeza ndipo khala mʼnyumba* mwako momwemo. Nʼchifukwa chiyani ukuputa tsoka chonsecho iwe ndi Ayudawo mugonja?”