2 Mafumu 14:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pa nkhondoyo, Ayuda anagonjetsedwa ndi Aisiraeli moti aliyense anathawira kunyumba* kwake.