-
2 Mafumu 14:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Nkhani zina zokhudza Yehoasi, zimene anachita, mphamvu zake komanso mmene anamenyanirana ndi Amaziya mfumu ya Yuda, zinalembedwa mʼbuku la mbiri ya mafumu a Isiraeli.
-