2 Mafumu 14:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kenako Yehoasi, mofanana ndi makolo ake, anamwalira ndipo anaikidwa mʼmanda ku Samariya+ pamodzi ndi mafumu a Isiraeli. Ndiyeno Yerobowamu*+ mwana wake anakhala mfumu mʼmalo mwake.
16 Kenako Yehoasi, mofanana ndi makolo ake, anamwalira ndipo anaikidwa mʼmanda ku Samariya+ pamodzi ndi mafumu a Isiraeli. Ndiyeno Yerobowamu*+ mwana wake anakhala mfumu mʼmalo mwake.