2 Mafumu 14:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Yehova anali ataona mavuto aakulu omwe Aisiraeli ankakumana nawo.+ Kunalibe aliyense woti akanawathandiza, ngakhale wooneka wonyozeka ndi wofooka.
26 Yehova anali ataona mavuto aakulu omwe Aisiraeli ankakumana nawo.+ Kunalibe aliyense woti akanawathandiza, ngakhale wooneka wonyozeka ndi wofooka.