2 Mafumu 14:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kenako Yerobowamu, mofanana ndi makolo ake, anamwalira nʼkuikidwa mʼmanda pamodzi ndi mafumu a Isiraeli ndipo mwana wake Zekariya+ anakhala mfumu mʼmalo mwake.
29 Kenako Yerobowamu, mofanana ndi makolo ake, anamwalira nʼkuikidwa mʼmanda pamodzi ndi mafumu a Isiraeli ndipo mwana wake Zekariya+ anakhala mfumu mʼmalo mwake.