2 Mafumu 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Azariya ankachita zoyenera pamaso pa Yehova ngati mmene anachitira Amaziya bambo ake.+