2 Mafumu 15:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova anachititsa khate mfumuyo moti inali yakhate+ mpaka tsiku lomwe inamwalira. Inkakhala mʼnyumba kwayokha+ ndipo mwana wake Yotamu+ ndi amene ankayangʼanira nyumba ya mfumu komanso kuweruza anthu amʼdzikolo.+ 2 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:5 Nsanja ya Olonda,4/15/2015, tsa. 218/1/2005, tsa. 11
5 Yehova anachititsa khate mfumuyo moti inali yakhate+ mpaka tsiku lomwe inamwalira. Inkakhala mʼnyumba kwayokha+ ndipo mwana wake Yotamu+ ndi amene ankayangʼanira nyumba ya mfumu komanso kuweruza anthu amʼdzikolo.+