2 Mafumu 15:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mʼchaka cha 38 cha Azariya+ mfumu ya Yuda, Zekariya+ mwana wa Yerobowamu anakhala mfumu ya Isiraeli ku Samariya ndipo analamulira miyezi 6.
8 Mʼchaka cha 38 cha Azariya+ mfumu ya Yuda, Zekariya+ mwana wa Yerobowamu anakhala mfumu ya Isiraeli ku Samariya ndipo analamulira miyezi 6.