2 Mafumu 15:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iye anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova ngati mmene anachitira makolo ake. Sanasiye kuchita machimo amene Aisiraeli ankachita chifukwa cha Yerobowamu mwana wa Nebati.+
9 Iye anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova ngati mmene anachitira makolo ake. Sanasiye kuchita machimo amene Aisiraeli ankachita chifukwa cha Yerobowamu mwana wa Nebati.+