2 Mafumu 15:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Izi zinakwaniritsa mawu amene Yehova anauza Yehu akuti: “Ana ako aamuna adzakhala pampando wachifumu wa Isiraeli+ mpaka mʼbadwo wa 4.”+ Ndipo zimenezi ndi zomwe zinachitikadi.
12 Izi zinakwaniritsa mawu amene Yehova anauza Yehu akuti: “Ana ako aamuna adzakhala pampando wachifumu wa Isiraeli+ mpaka mʼbadwo wa 4.”+ Ndipo zimenezi ndi zomwe zinachitikadi.