2 Mafumu 15:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Salumu mwana wa Yabesi, anakhala mfumu mʼchaka cha 39 cha Uziya+ mfumu ya Yuda. Iye analamulira ku Samariya kwa mwezi umodzi.
13 Salumu mwana wa Yabesi, anakhala mfumu mʼchaka cha 39 cha Uziya+ mfumu ya Yuda. Iye analamulira ku Samariya kwa mwezi umodzi.