2 Mafumu 15:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndiyeno Menahemu mwana wa Gadai, anachoka ku Tiriza+ kupita ku Samariya nʼkukapha Salumu+ mwana wa Yabesi ku Samariyako. Kenako iye anakhala mfumu mʼmalo mwake.
14 Ndiyeno Menahemu mwana wa Gadai, anachoka ku Tiriza+ kupita ku Samariya nʼkukapha Salumu+ mwana wa Yabesi ku Samariyako. Kenako iye anakhala mfumu mʼmalo mwake.